Deuteronomo 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ukapeza chisa cha mbalame mumtengo kapena pansi, muli ana+ kapena mazira, make atafungatira ana kapena mazirawo, usatenge make ndi ana omwe.+ Mateyu 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kodi mpheta ziwiri si paja amazigulitsa kakhobidi kamodzi kochepa mphamvu?+ Komatu palibe ngakhale imodzi imene idzagwa pansi Atate wanu osadziwa.+
6 “Ukapeza chisa cha mbalame mumtengo kapena pansi, muli ana+ kapena mazira, make atafungatira ana kapena mazirawo, usatenge make ndi ana omwe.+
29 Kodi mpheta ziwiri si paja amazigulitsa kakhobidi kamodzi kochepa mphamvu?+ Komatu palibe ngakhale imodzi imene idzagwa pansi Atate wanu osadziwa.+