Luka 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Imva tsopano! Udzakhala chete,+ osatha kulankhula mpaka tsiku limene zimenezi zidzachitike. Izi zidzachitika chifukwa sunakhulupirire mawu anga amene adzakwaniritsidwe pa nthawi yake yoikidwiratu.”
20 Imva tsopano! Udzakhala chete,+ osatha kulankhula mpaka tsiku limene zimenezi zidzachitike. Izi zidzachitika chifukwa sunakhulupirire mawu anga amene adzakwaniritsidwe pa nthawi yake yoikidwiratu.”