Mateyu 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Lowani pachipata chopapatiza.+ Pakuti msewu waukulu ndi wotakasuka ukupita kuchiwonongeko, ndipo anthu ambiri akuyenda mmenemo. Afilipi 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Si kuti ndalandira kale mphotoyo, kapena kuti ndakhala kale wangwiro+ ayi. Koma ndikuyesetsabe+ kuti ndione ngati inenso ndingapeze+ chimene chinachititsanso Khristu Yesu kundipeza.+
13 “Lowani pachipata chopapatiza.+ Pakuti msewu waukulu ndi wotakasuka ukupita kuchiwonongeko, ndipo anthu ambiri akuyenda mmenemo.
12 Si kuti ndalandira kale mphotoyo, kapena kuti ndakhala kale wangwiro+ ayi. Koma ndikuyesetsabe+ kuti ndione ngati inenso ndingapeze+ chimene chinachititsanso Khristu Yesu kundipeza.+