Zekariya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno mngeloyo anauza amene anaimirira pamaso pake kuti: “Muvuleni zovala zonyansazi.” Kenako anauza Yoswa kuti: “Waona, ndakuchotsera zolakwa zako,+ ndipo wavekedwa mikanjo yapadera.”+
4 Ndiyeno mngeloyo anauza amene anaimirira pamaso pake kuti: “Muvuleni zovala zonyansazi.” Kenako anauza Yoswa kuti: “Waona, ndakuchotsera zolakwa zako,+ ndipo wavekedwa mikanjo yapadera.”+