2 Samueli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Davide anauza+ Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+ 2 Mbiri 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Panali anthu ambiri ochokera ku Efuraimu,+ ku Manase,+ ku Isakara ndi ku Zebuloni+ amene sanadziyeretse+ ndipo anadya pasikayo mosatsatira zimene zinalembedwa.+ Koma Hezekiya anawapempherera+ kuti: “Yehova wabwino+ asakwiyire Salimo 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Wodala ndi munthu amene wakhululukidwa zolakwa zake, amene machimo ake aphimbidwa.+ Salimo 51:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikhululukireni machimo anga,+Ndipo fafanizani zolakwa zanga zonse.+ Aheberi 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ine ndidzawachitira chifundo pa zochita zawo zosalungama, ndipo sindidzakumbukiranso machimo awo.’”+
13 Pamenepo Davide anauza+ Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+
18 Panali anthu ambiri ochokera ku Efuraimu,+ ku Manase,+ ku Isakara ndi ku Zebuloni+ amene sanadziyeretse+ ndipo anadya pasikayo mosatsatira zimene zinalembedwa.+ Koma Hezekiya anawapempherera+ kuti: “Yehova wabwino+ asakwiyire
12 Ine ndidzawachitira chifundo pa zochita zawo zosalungama, ndipo sindidzakumbukiranso machimo awo.’”+