Mateyu 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Akam’pereka kwa anthu a mitundu ina kuti am’chitire chipongwe, kum’kwapula ndi kum’pachika pamtengo,+ ndipo pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+ Yohane 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiponso, monga mmene Mose anakwezera njoka m’mwamba+ m’chipululu, momwemonso Mwana wa munthu ayenera kukwezedwa m’mwamba,+ Yohane 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma ine ndikadzakwezedwa+ m’mwamba padziko lapansi, ndidzakokera anthu osiyanasiyana kwa ine.”+
19 Akam’pereka kwa anthu a mitundu ina kuti am’chitire chipongwe, kum’kwapula ndi kum’pachika pamtengo,+ ndipo pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+
14 Ndiponso, monga mmene Mose anakwezera njoka m’mwamba+ m’chipululu, momwemonso Mwana wa munthu ayenera kukwezedwa m’mwamba,+