Luka 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno anayamba kumuneneza+ kuti: “Ife tapeza munthu uyu akupandutsa+ mtundu wathu ndi kuletsa anthu kuti asamakhome msonkho+ kwa Kaisara, komanso iyeyu akunena kuti ndi Khristu mfumu.”+ Machitidwe 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ndipo Yasoni anawalandira bwino. Anthu onsewa akuchita zotsutsana ndi malamulo+ a Kaisara. Akunena kuti eti kulinso mfumu ina+ dzina lake Yesu.”
2 Ndiyeno anayamba kumuneneza+ kuti: “Ife tapeza munthu uyu akupandutsa+ mtundu wathu ndi kuletsa anthu kuti asamakhome msonkho+ kwa Kaisara, komanso iyeyu akunena kuti ndi Khristu mfumu.”+
7 ndipo Yasoni anawalandira bwino. Anthu onsewa akuchita zotsutsana ndi malamulo+ a Kaisara. Akunena kuti eti kulinso mfumu ina+ dzina lake Yesu.”