Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 95:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Pakuti iye ndi Mulungu wathu ndipo ife ndife anthu ake. Iye amatisamalira ngati nkhosa zimene akuweta.+

      Lero anthu inu mukamvera mawu a Mulungu,+

  • Mateyu 10:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 M’malomwake, nthawi zonse muzipita kwa nkhosa zosochera za nyumba ya Isiraeli.+

  • Machitidwe 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano m’masiku amenewa, Petulo anaimirira pakati pa abalewo (gulu lonselo linali la anthu pafupifupi 120) n’kunena kuti:

  • Machitidwe 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma Petulo anaimirira pamodzi ndi atumwi 11 aja.+ Iye analankhula nawo mokweza mawu kuti: “Anthu inu a m’Yudeya ndi inu nonse okhala m’Yerusalemu,+ dziwani ndi kutchera khutu ku zimene ndikufuna kukuuzani pano.

  • Aheberi 13:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano, Mulungu wamtendere,+ amene anaukitsa kwa akufa+ m’busa wamkulu+ wa nkhosa+ wokhala ndi magazi a pangano losatha,+ Ambuye wathu Yesu,

  • 1 Petulo 2:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pakuti munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa m’busa+ wanu ndi woyang’anira miyoyo yanu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena