Yohane 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+ Machitidwe 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwadzidzidzi kumwamba kunamveka mkokomo ngati wa mphepo yamphamvu, ndipo unadzaza m’nyumba yonse imene iwo anakhalamo.+ Aroma 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti mzimuwo+ umachitira umboni+ limodzi ndi mzimu wathu+ kuti ndife ana a Mulungu.+ 1 Akorinto 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi ndi munthu uti amene angadziwe za munthu kupatulapo mzimu+ umene uli mwa munthuyo? Momwemonso, palibe amene akudziwa zinthu za Mulungu, kupatulapo mzimu+ wa Mulungu.
17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+
2 Mwadzidzidzi kumwamba kunamveka mkokomo ngati wa mphepo yamphamvu, ndipo unadzaza m’nyumba yonse imene iwo anakhalamo.+
11 Kodi ndi munthu uti amene angadziwe za munthu kupatulapo mzimu+ umene uli mwa munthuyo? Momwemonso, palibe amene akudziwa zinthu za Mulungu, kupatulapo mzimu+ wa Mulungu.