Machitidwe 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamene Paulo anali kuwayembekezera ku Atene, mtima unamuwawa kwambiri+ poona kuti mumzindawo mwadzaza mafano. Aroma 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika ndi moyo wanga wonse polalikira uthenga wabwino wonena za Mwana wake, ndiye mboni yanga+ ya mmene ndimakutchulirani m’mapemphero anga nthawi zonse.+ 1 Akorinto 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi ndi munthu uti amene angadziwe za munthu kupatulapo mzimu+ umene uli mwa munthuyo? Momwemonso, palibe amene akudziwa zinthu za Mulungu, kupatulapo mzimu+ wa Mulungu.
16 Pamene Paulo anali kuwayembekezera ku Atene, mtima unamuwawa kwambiri+ poona kuti mumzindawo mwadzaza mafano.
9 Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika ndi moyo wanga wonse polalikira uthenga wabwino wonena za Mwana wake, ndiye mboni yanga+ ya mmene ndimakutchulirani m’mapemphero anga nthawi zonse.+
11 Kodi ndi munthu uti amene angadziwe za munthu kupatulapo mzimu+ umene uli mwa munthuyo? Momwemonso, palibe amene akudziwa zinthu za Mulungu, kupatulapo mzimu+ wa Mulungu.