Yohane 6:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Koma pali ena mwa inu amene sakukhulupirira.” Pakuti kuchokera pa chiyambi, Yesu anadziwa amene sanali kukhulupirira komanso amene adzamupereka.+
64 Koma pali ena mwa inu amene sakukhulupirira.” Pakuti kuchokera pa chiyambi, Yesu anadziwa amene sanali kukhulupirira komanso amene adzamupereka.+