Yohane 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo palibe munthu amene anakwera kumwamba+ koma Mwana wa munthu+ yekha, amene anatsika kuchokera kumwambako.+ Yohane 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Chifukwa ndinatsika kuchokera kumwamba+ kudzachita chifuniro cha iye amene anandituma, osati chifuniro changa.+ Yohane 8:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anawauza kuti: “Inu ndinu ochokera pansi pano, ine ndine wochokera kumwamba.+ Inu ndinu ochokera m’dziko lino,+ ine si wochokera m’dziko lino.+ Machitidwe 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atatsiriza kunena zimenezi, Mulungu anamunyamula kupita m’mlengalenga iwo akuonerera,+ ndipo mtambo unamuphimba moti sanathenso kumuona.+ Aefeso 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero iye anati: “Atakwera kumwamba anagwira anthu ukapolo ndipo anapereka mphatso za amuna.”+
13 Ndipo palibe munthu amene anakwera kumwamba+ koma Mwana wa munthu+ yekha, amene anatsika kuchokera kumwambako.+
38 Chifukwa ndinatsika kuchokera kumwamba+ kudzachita chifuniro cha iye amene anandituma, osati chifuniro changa.+
23 Iye anawauza kuti: “Inu ndinu ochokera pansi pano, ine ndine wochokera kumwamba.+ Inu ndinu ochokera m’dziko lino,+ ine si wochokera m’dziko lino.+
9 Atatsiriza kunena zimenezi, Mulungu anamunyamula kupita m’mlengalenga iwo akuonerera,+ ndipo mtambo unamuphimba moti sanathenso kumuona.+