Malaki 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Tamverani anthu inu! Tsiku la Yehova lalikulu ndi lochititsa mantha lisanafike,+ ndidzakutumizirani mneneri Eliya.+ Mateyu 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kaya mukhulupirira kapena ayi, Yohane ndiye ‘Eliya woyembekezeka kubwera uja.’+ Mateyu 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ophunzirawo anamufunsa kuti: “Nanga n’chifukwa chiyani alembi amanena kuti Eliya ayenera kubwera choyamba?”+ Maliko 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kunena za kubwera kwa Eliya,+ ine ndikukuuzani kuti iye anabwera kale, ndipo anam’chitira zilizonse zimene anafuna, mmenedi Malemba amanenera za iye.”+
5 “Tamverani anthu inu! Tsiku la Yehova lalikulu ndi lochititsa mantha lisanafike,+ ndidzakutumizirani mneneri Eliya.+
10 Koma ophunzirawo anamufunsa kuti: “Nanga n’chifukwa chiyani alembi amanena kuti Eliya ayenera kubwera choyamba?”+
13 Kunena za kubwera kwa Eliya,+ ine ndikukuuzani kuti iye anabwera kale, ndipo anam’chitira zilizonse zimene anafuna, mmenedi Malemba amanenera za iye.”+