Mateyu 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akhungu akuonanso,+ olumala+ akuyendayenda, akhate+ akuyeretsedwa ndipo ogontha+ akumva. Akufa+ akuukitsidwa, ndipo kwa aumphawi uthenga wabwino ukulengezedwa.+ Yohane 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yesu atamva zimenezi ananena kuti: “Kudwala kumeneku si kwa imfa chabe, koma n’kopatsa Mulungu ulemerero,+ kuti mwa kudwalako, Mwana wa Mulungu alemekezeke.”
5 Akhungu akuonanso,+ olumala+ akuyendayenda, akhate+ akuyeretsedwa ndipo ogontha+ akumva. Akufa+ akuukitsidwa, ndipo kwa aumphawi uthenga wabwino ukulengezedwa.+
4 Koma Yesu atamva zimenezi ananena kuti: “Kudwala kumeneku si kwa imfa chabe, koma n’kopatsa Mulungu ulemerero,+ kuti mwa kudwalako, Mwana wa Mulungu alemekezeke.”