Maliko 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa kundisiya ndekha, chifukwa Malemba amati, ‘Ndidzapha m’busa,+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+ Luka 12:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Musaope,+ kagulu ka nkhosa+ inu, chifukwa Atate wanu wavomereza kukupatsani ufumu.+
27 Tsopano Yesu anawauza kuti: “Nonsenu muthawa kundisiya ndekha, chifukwa Malemba amati, ‘Ndidzapha m’busa,+ ndipo nkhosa zidzabalalika.’+