Yobu 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kukangocha, wakupha amadzukaKupita kukapha wozunzika ndi wosauka,+Ndipo usiku iye amakhala wakuba.+ Mateyu 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Chenjerani ndi aneneri onyenga+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwawo ali mimbulu yolusa.+
14 Kukangocha, wakupha amadzukaKupita kukapha wozunzika ndi wosauka,+Ndipo usiku iye amakhala wakuba.+
15 “Chenjerani ndi aneneri onyenga+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwawo ali mimbulu yolusa.+