Luka 9:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Ndiyeno anawauza kuti: “Aliyense wolandira mwana wamng’ono uyu m’dzina langa walandiranso ine. Ndipo aliyense wolandira ine walandiranso amene anandituma ine.+ Pakuti aliyense wokhala ngati wamng’ono+ pakati pa nonsenu ndi amene ali wamkulu.”+ 1 Petulo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Osati mochita ufumu+ pa anthu amene ali cholowa chochokera kwa Mulungu,+ koma mukhale zitsanzo kwa gulu la nkhosa.+
48 Ndiyeno anawauza kuti: “Aliyense wolandira mwana wamng’ono uyu m’dzina langa walandiranso ine. Ndipo aliyense wolandira ine walandiranso amene anandituma ine.+ Pakuti aliyense wokhala ngati wamng’ono+ pakati pa nonsenu ndi amene ali wamkulu.”+
3 Osati mochita ufumu+ pa anthu amene ali cholowa chochokera kwa Mulungu,+ koma mukhale zitsanzo kwa gulu la nkhosa.+