Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+ Mateyu 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Taonani mtumiki wanga+ amene ndamusankha, wokondedwa wanga,+ amene moyo wanga ukukondwera naye. Ndidzaika mzimu wanga pa iye,+ ndipo adzasonyeza bwinobwino chilungamo chenicheni kwa anthu a mitundu ina. Yohane 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Wokhulupirira mwa iye sayenera kuweruzidwa.+ Wosakhulupirira waweruzidwa kale, chifukwa sanakhulupirire m’dzina la Mwana wobadwa yekha wa Mulungu.+
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndamugwiritsitsa,+ amene ndamusankha,+ ndiponso amene moyo wanga ukukondwera naye.+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye,+ ndipo iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+
18 “Taonani mtumiki wanga+ amene ndamusankha, wokondedwa wanga,+ amene moyo wanga ukukondwera naye. Ndidzaika mzimu wanga pa iye,+ ndipo adzasonyeza bwinobwino chilungamo chenicheni kwa anthu a mitundu ina.
18 Wokhulupirira mwa iye sayenera kuweruzidwa.+ Wosakhulupirira waweruzidwa kale, chifukwa sanakhulupirire m’dzina la Mwana wobadwa yekha wa Mulungu.+