Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “‘Tsiku limeneli lidzakhala chikumbutso kwa inu, ndipo muzichitira Yehova chikondwerero m’mibadwo yanu yonse. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale, kuti muzichita chikondwerero chimenechi.

  • Numeri 28:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “‘M’mwezi woyamba, pa tsiku la 14, pazikhala pasika wa Yehova.+

  • Deuteronomo 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Muzisunga mwambo wa m’mwezi wa Abibu*+ pochita chikondwerero cha pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa m’mwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+

  • Yohane 11:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Tsopano pasika+ wa Ayuda anali pafupi, ndipo anthu ochuluka anachoka m’midzi ndi kupita ku Yerusalemu pasikayo asanafike, kuti akachite mwambo wa kudziyeretsa.+

  • Yohane 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kutangotsala masiku 6 kuti pasika ayambike, Yesu anafika ku Betaniya+ kumene kunali Lazaro,+ uja amene Yesu anamuukitsa kwa akufa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena