Machitidwe 2:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pamenepo anthu onse anayamba kuchita mantha, ndipo atumwiwo anayamba kuchita zodabwitsa ndi zizindikiro zambiri.+ Machitidwe 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Hananiya atamva mawu amenewa anagwa pansi ndi kumwalira.+ Ndipo onse amene anamva zimenezi anagwidwa ndi mantha aakulu.+
43 Pamenepo anthu onse anayamba kuchita mantha, ndipo atumwiwo anayamba kuchita zodabwitsa ndi zizindikiro zambiri.+
5 Hananiya atamva mawu amenewa anagwa pansi ndi kumwalira.+ Ndipo onse amene anamva zimenezi anagwidwa ndi mantha aakulu.+