Machitidwe 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse mogwirizana anali kusonkhana m’khonde la zipilala la Solomo.+ Machitidwe 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Izi zinadziwika kwa onse, Ayuda ndi Agiriki amene anali kukhala ku Efeso. Chotero onse anagwidwa ndi mantha,+ ndipo dzina la Ambuye Yesu linapitirira kulemekezedwa.+
12 Choncho atumwiwo anapitiriza kuchita zizindikiro ndi zodabwitsa zambiri pakati pa anthu.+ Ndipo okhulupirira onse mogwirizana anali kusonkhana m’khonde la zipilala la Solomo.+
17 Izi zinadziwika kwa onse, Ayuda ndi Agiriki amene anali kukhala ku Efeso. Chotero onse anagwidwa ndi mantha,+ ndipo dzina la Ambuye Yesu linapitirira kulemekezedwa.+