Machitidwe 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anafika kwa ife ndi kutenga lamba wa Paulo. Kenako anadzimanga mapazi ndi manja ndi kunena kuti: “Mzimu woyera wati, ‘Mwiniwake wa lambayu, Ayuda adzamumanga+ chonchi ku Yerusalemu ndi kumupereka+ m’manja mwa anthu a mitundu ina.’” Machitidwe 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Titamva zimenezi, ife pamodzi ndi anthu akumeneko, tinayamba kuchonderera Paulo kuti asapite+ ku Yerusalemu.
11 Iye anafika kwa ife ndi kutenga lamba wa Paulo. Kenako anadzimanga mapazi ndi manja ndi kunena kuti: “Mzimu woyera wati, ‘Mwiniwake wa lambayu, Ayuda adzamumanga+ chonchi ku Yerusalemu ndi kumupereka+ m’manja mwa anthu a mitundu ina.’”
12 Titamva zimenezi, ife pamodzi ndi anthu akumeneko, tinayamba kuchonderera Paulo kuti asapite+ ku Yerusalemu.