Machitidwe 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chimodzi chokha chimene ndikudziwa n’chakuti mumzinda ndi mzinda, mzimu woyera+ wandichitira umboni mobwerezabwereza kuti maunyolo ndi masautso akundiyembekezera.+ Machitidwe 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pamenepo mkulu wa asilikali uja anafika pafupi ndi kumugwira ndipo analamula kuti amumange ndi maunyolo awiri.+ Ndiyeno anafunsa za iye kuti anali ndani ndiponso zimene anachita.
23 Chimodzi chokha chimene ndikudziwa n’chakuti mumzinda ndi mzinda, mzimu woyera+ wandichitira umboni mobwerezabwereza kuti maunyolo ndi masautso akundiyembekezera.+
33 Pamenepo mkulu wa asilikali uja anafika pafupi ndi kumugwira ndipo analamula kuti amumange ndi maunyolo awiri.+ Ndiyeno anafunsa za iye kuti anali ndani ndiponso zimene anachita.