Aroma 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti iye amene ali Myuda kunja kokha si Myuda ayi,+ ndiponso mdulidwe wakunja kokha wochitidwa pathupi, si mdulidwe ayi.+ 1 Akorinto 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mdulidwe+ sutanthauza kalikonse, ndipo kusadulidwa+ sikutanthauza kanthu, koma kusunga malamulo a Mulungu ndiko kofunika.+
28 Pakuti iye amene ali Myuda kunja kokha si Myuda ayi,+ ndiponso mdulidwe wakunja kokha wochitidwa pathupi, si mdulidwe ayi.+
19 Mdulidwe+ sutanthauza kalikonse, ndipo kusadulidwa+ sikutanthauza kanthu, koma kusunga malamulo a Mulungu ndiko kofunika.+