Mlaliki 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita. Yeremiya 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga,+ ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga. Muziyenda m’njira+ imene ndidzakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+ Agalatiya 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti kwa Khristu Yesu, kudulidwa kapena kusadulidwa zilibe phindu,+ koma chikhulupiriro+ chimene chimagwira ntchito kudzera m’chikondi.+ 1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+
13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.
23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga,+ ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga. Muziyenda m’njira+ imene ndidzakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+
6 Pakuti kwa Khristu Yesu, kudulidwa kapena kusadulidwa zilibe phindu,+ koma chikhulupiriro+ chimene chimagwira ntchito kudzera m’chikondi.+
3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+