1 Atesalonika 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Timatero pakuti timakumbukira nthawi zonse ntchito zanu zachikhulupiriro,+ ndi ntchito zanu zachikondi. Timateronso pokumbukira mmene munapiririra chifukwa cha chiyembekezo+ chanu mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, pamaso pa Mulungu wathu ndi Atate. 1 Timoteyo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndithu, cholinga chokulamulira zimenezi n’chakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera,+ m’chikumbumtima chabwino,+ ndiponso m’chikhulupiriro chopanda chinyengo.+
3 Timatero pakuti timakumbukira nthawi zonse ntchito zanu zachikhulupiriro,+ ndi ntchito zanu zachikondi. Timateronso pokumbukira mmene munapiririra chifukwa cha chiyembekezo+ chanu mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, pamaso pa Mulungu wathu ndi Atate.
5 Ndithu, cholinga chokulamulira zimenezi n’chakuti tikhale ndi chikondi+ chochokera mumtima woyera,+ m’chikumbumtima chabwino,+ ndiponso m’chikhulupiriro chopanda chinyengo.+