Machitidwe 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndi wodziwika bwino kwa Ayuda amene andidziwa ine kuchokera kale. Ndipo atafuna, angandichitire umboni kuti ndinalidi Mfarisi,+ wa m’gulu lampatuko lotsatira kulambira kwathu mokhwimitsa zinthu kwambiri.+ Afilipi 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ineyo ndinadulidwa pa tsiku la 8,+ ndine wa mtundu wa Isiraeli, wa fuko la Benjamini,+ Mheberi wobadwa kwa Aheberi.+ Kunena za chilamulo, ndine Mfarisi.+
5 Ndi wodziwika bwino kwa Ayuda amene andidziwa ine kuchokera kale. Ndipo atafuna, angandichitire umboni kuti ndinalidi Mfarisi,+ wa m’gulu lampatuko lotsatira kulambira kwathu mokhwimitsa zinthu kwambiri.+
5 Ineyo ndinadulidwa pa tsiku la 8,+ ndine wa mtundu wa Isiraeli, wa fuko la Benjamini,+ Mheberi wobadwa kwa Aheberi.+ Kunena za chilamulo, ndine Mfarisi.+