9 Ndiyeno panafika amuna ena a gulu lotchedwa Sunagoge wa Omasulidwa, ndi ena a ku Kurene, a ku Alekizandiriya,+ komanso ena ochokera ku Kilikiya+ ndi ku Asia, kudzatsutsana ndi Sitefano.
39 Pamenepo Paulo ananena kuti: “Inetu ndine Myuda+ wa ku Tariso,+ ku Kilikiya, nzika ya mzinda wotchuka. Chonde ndikukupemphani, kuti mundilole ndilankhule kwa anthuwa.”