Machitidwe 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ambuyewo anamuuza kuti: “Nyamuka, upite kumsewu wotchedwa Msewu Wowongoka. Ukakafika panyumba ya Yudasi, ukafunse za munthu wa ku Tariso, dzina lake Saulo.+ Iyeyo akupemphera, Machitidwe 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Inetu ndine Myuda,+ wobadwira ku Tariso wa ku Kilikiya,+ koma ndinaphunzitsidwa ndi Gamaliyeli+ mumzinda womwe uno. Anandiphunzitsa kutsatira Chilamulo cha makolo athu mokhwimitsa zinthu kwambiri.+ Ndipo ndinali wodzipereka+ potumikira Mulungu monga mmene nonsenu mulili lero.
11 Ambuyewo anamuuza kuti: “Nyamuka, upite kumsewu wotchedwa Msewu Wowongoka. Ukakafika panyumba ya Yudasi, ukafunse za munthu wa ku Tariso, dzina lake Saulo.+ Iyeyo akupemphera,
3 “Inetu ndine Myuda,+ wobadwira ku Tariso wa ku Kilikiya,+ koma ndinaphunzitsidwa ndi Gamaliyeli+ mumzinda womwe uno. Anandiphunzitsa kutsatira Chilamulo cha makolo athu mokhwimitsa zinthu kwambiri.+ Ndipo ndinali wodzipereka+ potumikira Mulungu monga mmene nonsenu mulili lero.