Machitidwe 21:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pamenepo Paulo ananena kuti: “Inetu ndine Myuda+ wa ku Tariso,+ ku Kilikiya, nzika ya mzinda wotchuka. Chonde ndikukupemphani, kuti mundilole ndilankhule kwa anthuwa.” Machitidwe 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho iye anaiwerenga ndi kufunsa chigawo chimene anali kuchokera, ndipo anapeza kuti+ ndi wochokera ku Kilikiya.+
39 Pamenepo Paulo ananena kuti: “Inetu ndine Myuda+ wa ku Tariso,+ ku Kilikiya, nzika ya mzinda wotchuka. Chonde ndikukupemphani, kuti mundilole ndilankhule kwa anthuwa.”
34 Choncho iye anaiwerenga ndi kufunsa chigawo chimene anali kuchokera, ndipo anapeza kuti+ ndi wochokera ku Kilikiya.+