Machitidwe 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndi wodziwika bwino kwa Ayuda amene andidziwa ine kuchokera kale. Ndipo atafuna, angandichitire umboni kuti ndinalidi Mfarisi,+ wa m’gulu lampatuko lotsatira kulambira kwathu mokhwimitsa zinthu kwambiri.+ Aroma 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu! Paja inenso ndine Mwisiraeli,+ wa mbewu ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.+
5 Ndi wodziwika bwino kwa Ayuda amene andidziwa ine kuchokera kale. Ndipo atafuna, angandichitire umboni kuti ndinalidi Mfarisi,+ wa m’gulu lampatuko lotsatira kulambira kwathu mokhwimitsa zinthu kwambiri.+
11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu! Paja inenso ndine Mwisiraeli,+ wa mbewu ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.+