Agalatiya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinali kupita patsogolo kwambiri m’Chiyuda kuposa anzanga ambiri a fuko langa, omwe anali amsinkhu wanga.+ Pakuti ndinali wodzipereka kwambiri+ pa miyambo+ ya makolo anga. Afilipi 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kunena za kudzipereka, ndinali kuzunza mpingo.+ Kunena za chilungamo mwa kutsatira chilamulo, ndinakhaladi wopanda chifukwa chondinenezera.
14 Ndinali kupita patsogolo kwambiri m’Chiyuda kuposa anzanga ambiri a fuko langa, omwe anali amsinkhu wanga.+ Pakuti ndinali wodzipereka kwambiri+ pa miyambo+ ya makolo anga.
6 Kunena za kudzipereka, ndinali kuzunza mpingo.+ Kunena za chilungamo mwa kutsatira chilamulo, ndinakhaladi wopanda chifukwa chondinenezera.