Machitidwe 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma pamene Paulo anapempha+ kuti timusunge kuti akamve chigamulo cha Wolemekezeka, ndinalamula kuti asungidwe mpaka pamene ndidzamutumize kwa Kaisara.” Machitidwe 26:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo Agiripa anauza Fesito kuti: “Akanakhala kuti sanapemphe kukaonekera kwa Kaisara, munthu ameneyu akanamasulidwa ndithu.”+ Machitidwe 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Ayuda atapitiriza kutsutsa zimenezo, ndinakakamizika kupempha+ kudzaonekera kwa Kaisara, komatu sikuti ndinali ndi kanthu koti ndidzaneneze mtundu wanga ayi.
21 Koma pamene Paulo anapempha+ kuti timusunge kuti akamve chigamulo cha Wolemekezeka, ndinalamula kuti asungidwe mpaka pamene ndidzamutumize kwa Kaisara.”
32 Ndipo Agiripa anauza Fesito kuti: “Akanakhala kuti sanapemphe kukaonekera kwa Kaisara, munthu ameneyu akanamasulidwa ndithu.”+
19 Koma Ayuda atapitiriza kutsutsa zimenezo, ndinakakamizika kupempha+ kudzaonekera kwa Kaisara, komatu sikuti ndinali ndi kanthu koti ndidzaneneze mtundu wanga ayi.