Miyambo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkwiyo umasefukira ndipo ukali ndi wankhanza,+ koma nsanje ndani angaipirire?+ Mateyu 27:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti iye anadziwa kuti anamupereka chifukwa cha kaduka.+