Machitidwe 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma mawu+ a Yehova anapitiriza kukula ndi kufalikira.+ Machitidwe 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho mawu a Yehova anapitiriza kufalikira ndi kugonjetsa zopinga zambiri.+