Yesaya 55:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+ Machitidwe 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo mawu a Mulungu anapitiriza kufalikira ponseponse.+ Chiwerengero cha ophunzira chinali kuwonjezeka kwambiri mu Yerusalemu.+ Ndipo ansembe ambirimbiri+ anakhala okhulupirira.+ Machitidwe 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho mawu a Yehova anapitiriza kufalikira ndi kugonjetsa zopinga zambiri.+
11 ndi mmenenso adzakhalire mawu otuluka pakamwa panga.+ Sadzabwerera kwa ine popanda kukwaniritsa cholinga chake,+ koma adzachitadi zimene ine ndikufuna+ ndipo adzakwaniritsadi zimene ndinawatumizira.+
7 Pamenepo mawu a Mulungu anapitiriza kufalikira ponseponse.+ Chiwerengero cha ophunzira chinali kuwonjezeka kwambiri mu Yerusalemu.+ Ndipo ansembe ambirimbiri+ anakhala okhulupirira.+