Yohane 12:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Komabe ambiri, ngakhalenso olamulira anamukhulupirira,+ koma chifukwa cha Afarisi sanavomereze poyera, poopa kuti angawachotse musunagoge.+ Machitidwe 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma okhulupirira ena, amene kale anali m’gulu lampatuko la Afarisi anaimirira m’mipando yawo n’kunena kuti: “M’pofunika kuwadula+ ndi kuwalamula kuti azisunga chilamulo cha Mose.”+
42 Komabe ambiri, ngakhalenso olamulira anamukhulupirira,+ koma chifukwa cha Afarisi sanavomereze poyera, poopa kuti angawachotse musunagoge.+
5 Koma okhulupirira ena, amene kale anali m’gulu lampatuko la Afarisi anaimirira m’mipando yawo n’kunena kuti: “M’pofunika kuwadula+ ndi kuwalamula kuti azisunga chilamulo cha Mose.”+