Machitidwe 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo mawu a Mulungu anapitiriza kufalikira ponseponse.+ Chiwerengero cha ophunzira chinali kuwonjezeka kwambiri mu Yerusalemu.+ Ndipo ansembe ambirimbiri+ anakhala okhulupirira.+ Machitidwe 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma mawu+ a Yehova anapitiriza kukula ndi kufalikira.+ Akolose 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Uthenga wabwinowu unafika kwa inu popeza ukubala zipatso+ ndipo ukuwonjezeka+ m’dziko lonse.+ Ukuteronso pakati panu, kuyambira tsiku limene munamva ndi kudziwa molondola za kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu monga mmene kulilidi.+
7 Pamenepo mawu a Mulungu anapitiriza kufalikira ponseponse.+ Chiwerengero cha ophunzira chinali kuwonjezeka kwambiri mu Yerusalemu.+ Ndipo ansembe ambirimbiri+ anakhala okhulupirira.+
6 Uthenga wabwinowu unafika kwa inu popeza ukubala zipatso+ ndipo ukuwonjezeka+ m’dziko lonse.+ Ukuteronso pakati panu, kuyambira tsiku limene munamva ndi kudziwa molondola za kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu monga mmene kulilidi.+