Mateyu 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ndi kuwaphunzitsa+ kusunga+ zinthu zonse zimene ndinakulamulirani.+ Ndipo dziwani kuti ine ndili pamodzi ndi inu+ masiku onse mpaka m’nyengo ya mapeto a nthawi* ino.”+ Luka 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kutacha, anaitana ophunzira ake ndi kusankha 12 pakati pawo. Amenewa anawatcha “atumwi.”+ Yohane 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inu simunandisankhe ine, koma ine ndinakusankhani. Ndinakuikani kuti mupitirize kubala zipatso zochuluka,+ ndi kutinso zipatso zanuzo zisathe, kuti chilichonse chimene mungapemphe Atate m’dzina langa akupatseni.+
20 ndi kuwaphunzitsa+ kusunga+ zinthu zonse zimene ndinakulamulirani.+ Ndipo dziwani kuti ine ndili pamodzi ndi inu+ masiku onse mpaka m’nyengo ya mapeto a nthawi* ino.”+
16 Inu simunandisankhe ine, koma ine ndinakusankhani. Ndinakuikani kuti mupitirize kubala zipatso zochuluka,+ ndi kutinso zipatso zanuzo zisathe, kuti chilichonse chimene mungapemphe Atate m’dzina langa akupatseni.+