Ekisodo 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Yehova anachititsa Aiguputo kukomera mtima Aisiraeli.+ Nayenso Mose analemekezeka kwambiri m’dziko la Iguputo, pamaso pa atumiki a Farao ndi pamaso pa Aiguputo onse.+ Luka 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anawafunsa kuti: “Zinthu zotani?” Iwo anamuuza kuti: “Zinthu zokhudza Yesu Mnazareti,+ amene anali mneneri+ wamphamvu m’ntchito ndi m’mawu pamaso pa Mulungu ndi anthu onse.
3 Pamenepo Yehova anachititsa Aiguputo kukomera mtima Aisiraeli.+ Nayenso Mose analemekezeka kwambiri m’dziko la Iguputo, pamaso pa atumiki a Farao ndi pamaso pa Aiguputo onse.+
19 Iye anawafunsa kuti: “Zinthu zotani?” Iwo anamuuza kuti: “Zinthu zokhudza Yesu Mnazareti,+ amene anali mneneri+ wamphamvu m’ntchito ndi m’mawu pamaso pa Mulungu ndi anthu onse.