Ekisodo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mulungu anati: “Usayandikire kuno. Vula nsapato zako, chifukwa malo waimawo ndi malo oyera.”+ Yoswa 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno kalonga wa gulu lankhondo la Yehovayo anauza Yoswa kuti: “Vula nsapato zako, chifukwa malo amene waimapowo ndi oyera.” Nthawi yomweyo, Yoswa anavula nsapato zake.+
5 Ndiyeno Mulungu anati: “Usayandikire kuno. Vula nsapato zako, chifukwa malo waimawo ndi malo oyera.”+
15 Ndiyeno kalonga wa gulu lankhondo la Yehovayo anauza Yoswa kuti: “Vula nsapato zako, chifukwa malo amene waimapowo ndi oyera.” Nthawi yomweyo, Yoswa anavula nsapato zake.+