Yoswa 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno kalonga wa gulu lankhondo la Yehovayo anauza Yoswa kuti: “Vula nsapato zako, chifukwa malo amene waimapowo ndi oyera.” Nthawi yomweyo, Yoswa anavula nsapato zake.+ Machitidwe 7:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yehova anamuuza kuti, ‘Vula nsapato zako, pakuti malo amene waimawo ndi malo oyera.+
15 Ndiyeno kalonga wa gulu lankhondo la Yehovayo anauza Yoswa kuti: “Vula nsapato zako, chifukwa malo amene waimapowo ndi oyera.” Nthawi yomweyo, Yoswa anavula nsapato zake.+