Machitidwe 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Saulo anayamba kuzunza mpingo mwankhanza. Anali kulowa m’nyumba ndi nyumba, ndi kukokera panja amuna ndi akazi omwe, n’kukawaponya m’ndende.+ Agalatiya 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munamva ndithu zimene ndinali kuchita ndili m’Chiyuda,+ kuti ndinkazunza kwambiri+ mpingo wa Mulungu ndi kupitirizabe kuuwononga.+ Agalatiya 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo ankangomva kuti: “Munthu amene anali kutizunza kale uja,+ tsopano akulengeza uthenga wabwino wonena za chikhulupiriro chimene anali kuwononga.”+
3 Tsopano Saulo anayamba kuzunza mpingo mwankhanza. Anali kulowa m’nyumba ndi nyumba, ndi kukokera panja amuna ndi akazi omwe, n’kukawaponya m’ndende.+
13 Munamva ndithu zimene ndinali kuchita ndili m’Chiyuda,+ kuti ndinkazunza kwambiri+ mpingo wa Mulungu ndi kupitirizabe kuuwononga.+
23 Iwo ankangomva kuti: “Munthu amene anali kutizunza kale uja,+ tsopano akulengeza uthenga wabwino wonena za chikhulupiriro chimene anali kuwononga.”+