Machitidwe 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano Baranaba+ ndi Saulo atamaliza utumiki wopereka thandizo+ ku Yerusalemu, anabwerera ndi kutenga Yohane,+ wotchedwanso Maliko. Agalatiya 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno patapita zaka 14, ndinapita ku Yerusalemu kachiwiri+ limodzi ndi Baranaba,+ ndipo ndinatenganso Tito.
25 Tsopano Baranaba+ ndi Saulo atamaliza utumiki wopereka thandizo+ ku Yerusalemu, anabwerera ndi kutenga Yohane,+ wotchedwanso Maliko.
2 Ndiyeno patapita zaka 14, ndinapita ku Yerusalemu kachiwiri+ limodzi ndi Baranaba,+ ndipo ndinatenganso Tito.