Ekisodo 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kudya kwake mudzadye motere, mudzakhale mutamangirira m’chiuno mwanu,+ mutavala nsapato+ ndiponso mutatenga ndodo m’dzanja lanu. Muzidzadya mofulumira. Ameneyu ndi pasika* wa Yehova.+
11 Kudya kwake mudzadye motere, mudzakhale mutamangirira m’chiuno mwanu,+ mutavala nsapato+ ndiponso mutatenga ndodo m’dzanja lanu. Muzidzadya mofulumira. Ameneyu ndi pasika* wa Yehova.+