Machitidwe 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Woyang’anira ndende uja atadzuka ku tulo take ndi kuona kuti zitseko za ndende n’zotseguka, anasolola lupanga lake kuti adziphe,+ poganiza kuti akaidiwo athawa.+
27 Woyang’anira ndende uja atadzuka ku tulo take ndi kuona kuti zitseko za ndende n’zotseguka, anasolola lupanga lake kuti adziphe,+ poganiza kuti akaidiwo athawa.+