Salimo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti simudzasiya moyo wanga m’Manda.+Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.+ Machitidwe 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho pokhala mneneri, iye anaoneratu zapatsogolo ndi kuneneratu za kuuka kwa Khristu. Ananeneratu kuti iye sanasiyidwe m’Manda, komanso kuti thupi lake silinavunde.+
31 Choncho pokhala mneneri, iye anaoneratu zapatsogolo ndi kuneneratu za kuuka kwa Khristu. Ananeneratu kuti iye sanasiyidwe m’Manda, komanso kuti thupi lake silinavunde.+