Machitidwe 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipo anachitadi zimenezo mwa kutumiza thandizolo kwa akulu, kudzera mwa Baranaba ndi Saulo.+ Machitidwe 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Popitiriza ulendo wawo m’mizinda, anali kupatsa okhulupirira a kumeneko malamulo oyenera kuwatsatira, malinga ndi zimene atumwi ndi akulu ku Yerusalemu anagamula.+ Agalatiya 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno patapita zaka 14, ndinapita ku Yerusalemu kachiwiri+ limodzi ndi Baranaba,+ ndipo ndinatenganso Tito.
4 Popitiriza ulendo wawo m’mizinda, anali kupatsa okhulupirira a kumeneko malamulo oyenera kuwatsatira, malinga ndi zimene atumwi ndi akulu ku Yerusalemu anagamula.+
2 Ndiyeno patapita zaka 14, ndinapita ku Yerusalemu kachiwiri+ limodzi ndi Baranaba,+ ndipo ndinatenganso Tito.