-
Machitidwe 13:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Chotero amuna awa, amene mzimu woyera unawatumiza, anapita ku Selukeya, ndipo kuchokera kumeneko ananyamuka ulendo wa pamadzi wopita ku Kupuro.
-