1 Atesalonika 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, pamene ndili limodzi ndi Silivano+ ndi Timoteyo,+ ndikulembera mpingo wa Atesalonika wogwirizana+ ndi Mulungu Atate ndi Ambuye Yesu Khristu, kuti: Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere+ zikhale nanu. 1 Petulo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndakulemberani m’mawu ochepa kudzera mwa Silivano,+ m’bale amene ndikumuona kuti ndi wokhulupirika. Ndakulemberani zimenezi+ kuti ndikulimbikitseni ndi kupereka umboni wamphamvu wakuti kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu n’kumeneku, ndipo mukugwire mwamphamvu.+
1 Ine Paulo, pamene ndili limodzi ndi Silivano+ ndi Timoteyo,+ ndikulembera mpingo wa Atesalonika wogwirizana+ ndi Mulungu Atate ndi Ambuye Yesu Khristu, kuti: Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere+ zikhale nanu.
12 Ndakulemberani m’mawu ochepa kudzera mwa Silivano,+ m’bale amene ndikumuona kuti ndi wokhulupirika. Ndakulemberani zimenezi+ kuti ndikulimbikitseni ndi kupereka umboni wamphamvu wakuti kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu n’kumeneku, ndipo mukugwire mwamphamvu.+